| Nduna yoona nkhani zakunja kwa Pakistan yatsutsa zakuti boma lake likulekelera achifwamba amene |
|
|
 |
| |
..akudumpha malire ndi kukachita za upandu mu Afghanistan: Chouchi Kasouri wati boma lake lachitidwila nkhanza ndi achifwamba kuposa zimene bungwe la NATO ndi America achitodwila.
|
| |
Read more |
| |
| Mtsogoleri wakale wa America Clinton wakhalira kumbuyo Obama kuti ayimilire chipani cha Democrat |
|
Thu, 28 August 2008
|
 |
| |
Mtsogoleri wakale wa America Clinton wakhalira kumbuyo Obama kuti ayimilire chipani cha Democrat pa masankho a president ku America
|
| |
Read more |
| |
| Boma la Egypt lamanga mzika 33 za Africa zimene zimafuna kupita ku Israel mwa mbanda |
|
Thu, 28 August 2008
|
 |
| |
Boma la Egypt lamanga mzika 33 za Africa zimene zimafuna kupita ku Israel mwa mbanda. Mgululi mulinso ana anayi
|
| |
Read more |
| |
| Magulu achifwamba ndi kupelewela kwa zipangizo pakati pa asilikali osungitsa mtendere zikusokoneza n |
|
Fri, 15 August 2008
|
 |
| |
Bungwe la United Nations lati ncthito yake yosungitsa mtendere ku DRC ikusokonekela chifukwa asilikali ake osungitsa mtendere alibe zipangizo zokwanila ndiponso chifukwa cha magulu achifwamba.
|
| |
Read more |
| |
| Police ya Egypt yagwila gulu limene limazembetsa achinyamata a mdzikomo kupita ku Ulaya |
|
Thu, 14 August 2008
|
 |
| |
Police ya Egypt yagwila gulu limene limazembetsa achinyamata a mdzikomo kupita ku Ulaya. Gululi limanyenga boma kuti likutenga achinyamata kukachita maphunziro apadera a masewero olimbitsa thupi.
|
| |
Read more |
| |
| |