| Search:
|
|
|
| |
|
| |
|
|
| Partnership Links
|
|
|
|
 |
--Kumwela kwa chipululu cha sahara |
|
| Achifwamba amasula mkulu wa nthambi ya United Nations ku Somalia amene anamugwila momukakamiza |
|
Thu, 28 August 2008
|
 |
| |
Achifwamba amasula mkulu wa nthambi ya United Nations ku Somalia amene anamugwila momukakamiza
|
| |
Read more |
| |
| Zigawenga zaku Darfur zadzudzula boma kuti lakwimitsa nkhondo yoputa madera a zigawenga |
|
Thu, 14 August 2008
|
 |
| |
Zigawenga zaku Darfur zadzudzula boma la Sudan kuti lakhwimitsa nkhondo yoputa madera amene ali mmanja mwao. Kwa nthawi yoyamba magulu a zigawenga zakugonja ku madera aku mpoto kwa Darfur.
|
| |
Read more |
| |
| Asilikali a Sierra Leone anaphulitsa utsi okhetsa misonzi kubalalitsa anthu ochita zionetsero |
|
Thu, 14 August 2008
|
 |
| |
Asilikali a Sierra Leone anaphulitsa utsi okhetsa mizonzi kubalalitsa anthu ochita zionetsero. Anthuwa anazungulira office ya office ya chipani chotsutsa cha People’s Party.
|
| |
Read more |
| |
| Mkulu wa bwalo laza milandu lapa dziko lonse wati adula dzisamani dzoimba milandu akuluakulu a magul |
|
Fri, 18 July 2008
|
 |
| |
Mkulu wa bwalo laza milandu lapa dziko lonse la ICC, Luis Moreno-Ocampo, wati adula dzisamani dzoimba milandu akuluakulu a magulu azigawenga ku Darfur.
|
| |
Read more |
| |
| Albani watumiza asilikali okakhala nawo mgulu losungitsa mtendere ku Chad |
|
Fri, 18 July 2008
|
 |
| |
Boma la Albania latumiza asilikali 62 okakhala nawo mgulu la asilikali a European Union osungitsa mtendere ku Chad.
|
| |
Read more |
| |
| |
|
|
|
|