| Mtsogoleri wa gulu la zigawenga ku Sudan wati apitilira kuputa mzdinda wa Khartoum |
|
Mon, 12 May 2008
|
 |
| |
Mtsogoleri wa gulu la zigawenga la Justice and Equality Movement – JEM- ku Sudan wati apitilira kuputa mzinda wa Khartoum mpaka boma la dzikolo litagwa
|
| |
Read more |
| |
| Maiko a DRC ndi Uganda apempha mtsogoleri wa LRA kuti asaine pangano la mtendere |
|
Mon, 12 May 2008
|
 |
| |
Maiko a DRC ndi Uganda apempha mtsogoleri wa gulu la zigawenga la Lords Resistance Army kuti asaine pangano la mtendere
|
| |
Read more |
| |
| Mtsogoleri wa Lords Resistance Army wakana kukumana ndi akazembe a maiko akunja |
|
Mon, 21 April 2008
|
 |
| |
Mtsogoleri wa gulu la zigwenga la Lords Resistance Army wakana kukumana ndi akazembe a maiko akunja.
|
| |
Read more |
| |
| Gulu lachifwamba mothandizidwa ndi boma la Sudan lapha anthu wamba oposa makumi awiri mmudzi |
|
Mon, 28 January 2008
|
 |
| |
Gulu lachifwamba mothandizidwa ndi boma la Sudan lapha anthu wamba oposa makumi awiri mmudzi wa mchigawo cha Darfur
|
| |
Read more |
| |
| Mulandu wa mtsogoleri wakale wa Liberia wayambika ku Liberia |
|
Mon, 7 January 2008
|
 |
| |
Mulandu wa mtsogoleri wakale wa Liberia wayambika ku Liberia. Akuluakulu a bwalo ati mulanduwu ukhala mulingo woona momwe milandu ina yotere ingadzayendele mtsogolo muno.
|
| |
Read more |
| |
| |