Search:
 



 




Partnership Links
--Zamalonda  






Mtsogoleri wa Zambia wati akuganiza zosintha za malamulo okumbila mwala wa copper
Mon, 14 January 2008
  Mtsogoleri wa Zambia wati akuganiza zosintha za malamulo okumbila mwala wa copper mdziokomo.
  Read more
 
Mtengo wa chimanga mu South Africa watsika pamene mvula ikugwa bwino
Mon, 14 January 2008
  Mtengo wa chimanga mu South Africa watsika pamene mvula ikugwa bwino. Koma kutsika mtengo kwa chimanga kuchititsa kuti anthu ambiri athamangile kukagula.
  Read more
 
Bungwe loona za macompany ndi maiko akunja okayambitsa ntchito za chuma mu Zimbabwe lati linabvomele
Mon, 14 January 2008
  Bungwe loona za macompany ndi maiko akunja okayambitsa ntchito za chuma mu Zimbabwe lati linabvomeleza ntchito za ndalama zokwana 7.8 billion dollars zakuti akunja akayambitse mdzikomo
  Read more
 
Boma la Benin lapempha anthu a nthcito za business amu South Africa kuti akayembitse ntchito
Mon, 5 March 2007
  ..zawo mdzikomo: Nduna yoona nkhani zakunja ku Benin maryana Diallo Boni yati ma South Africa angakayambitse ntchito za zomangamanga, za luso la makono ndi za maulendo apa ndege.
  Read more
 
Mtolankhani wodziwika bwino pa kanema ndi katswiri oyimba akuchemelera malonda a zobvala
Fri, 13 October 2006
  ..zimene ndalama zake zidzathandiza kulimbana ndi matenda a Aids: Mtolankhani wodziwika bwino pa kanema, Oprah Winfrey ndi katswiri woimba Bono anapita kukagula zogulagula mu mzinda wa Chicago.
  Read more
 
 
Bwelelani kuchiyambi  |  Bungwe la SABC  |  SABC News  |  SABC Africa  |  Cholinga ndi masomphenya  |  Ngodya zathu  |  Malamulo    Mmene mungatipezele  |  Za channel africa  |  Maganizo anu  |  Tsamba lathup
© Tiletsa kukopera izi 1999 -2001 Channel Africa.