Search:
 



 




Partnership Links
--Zapadziko  






Nduna yoona nkhani zakunja kwa Pakistan yatsutsa zakuti boma lake likulekelera achifwamba amene
  ..akudumpha malire ndi kukachita za upandu mu Afghanistan: Chouchi Kasouri wati boma lake lachitidwila nkhanza ndi achifwamba kuposa zimene bungwe la NATO ndi America achitodwila.
  Read more
 
Chibvomezi chagunduza kumadzulo kwa China
Mon, 12 May 2008
  Chibvomelezi chagunduza kumadzulo kwa dziko la China. Chibvomezichi chakukhudza dela la Sichuan limene liri makilometre 92 kuchoka mu mzinda wa Chengdu
  Read more
 
Police ya Spain yamanga anthu awiri amene akuwaganizila kuti ndi asilamu a ganyavu
Wed, 2 April 2008
 
  Read more
 
America wauza a United Nations kuti atumize asilikali ku Darfur
Wed, 2 April 2008
  America wauza bungwe la United Nations kuti litumize asilikali 3 600 okasungitsa mtendere ku Darfur pokwana mwezi wa June
  Read more
 
Nduna yaikulu ya Britain yati siinaletse wina aliyense kukakhala nawo pa msonkhano wa
Mon, 22 October 2007
  ..atsogoleri a maiko amu Africa ndi ku Ulaya: Nduna yaikulu ya Britain yauza mtsogoleri wa South Africa kuti sanaletse wina aliyense kukakhala nawo pa msonkhano wa atsogoleri a maiko aku Ulaya ndi Africa.
  Read more
 
 
Bwelelani kuchiyambi  |  Bungwe la SABC  |  SABC News  |  SABC Africa  |  Cholinga ndi masomphenya  |  Ngodya zathu  |  Malamulo    Mmene mungatipezele  |  Za channel africa  |  Maganizo anu  |  Tsamba lathup
© Tiletsa kukopera izi 1999 -2001 Channel Africa.