Search:
 



 




Partnership Links
--Africa  






Mtsogoleri wotsutsa boma ku Zimbabwe wati akufuna chitsimikizo cha chitetezo asanabwelere kwao
Mon, 12 May 2008
  Mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma ku Zimbabwe, Morgan Tsvangirai wati akufuna kuti maiko a SADC amutsimikizile za chitetezo chake asanabwelere kwao
  Read more
 
Mtsogoleri wa gulu la zigawenga ku Sudan wati apitilira kuputa mzdinda wa Khartoum
Mon, 12 May 2008
  Mtsogoleri wa gulu la zigawenga la Justice and Equality Movement – JEM- ku Sudan wati apitilira kuputa mzinda wa Khartoum mpaka boma la dzikolo litagwa
  Read more
 
Mtsogoleri wa Lords Resistance Army wakana kukumana ndi akazembe a maiko akunja
Mon, 21 April 2008
  Mtsogoleri wa gulu la zigwenga la Lords Resistance Army wakana kukumana ndi akazembe a maiko akunja.
  Read more
 
Bungwe loimila apa ntchito lati lipempha mabungwe kuti ayimitse sitima yonyamula zida zaku Zimbabwe
Mon, 21 April 2008
  Bungwe loimila anthu apa ntchito mu South Africa la Trade and Allied Workers –SATAWU- lati lipempha maiko ndi mabungwe apa dziko kuti ayimitse sitima yapa madzi yaku China
  Read more
 
Police ya Spain yamanga anthu awiri amene akuwaganizila kuti ndi asilamu a ganyavu
Wed, 2 April 2008
 
  Read more
 
 
Bwelelani kuchiyambi  |  Bungwe la SABC  |  SABC News  |  SABC Africa  |  Cholinga ndi masomphenya  |  Ngodya zathu  |  Malamulo    Mmene mungatipezele  |  Za channel africa  |  Maganizo anu  |  Tsamba lathup
© Tiletsa kukopera izi 1999 -2001 Channel Africa.