Search:
 



 




Partnership Links
Bwelelani kuchiyambi  
Mtsogoleri wotsutsa boma ku Zimbabwe wati akufuna chitsimikizo cha chitetezo asanabwelere kwao
Mon, 12 May 2008
Mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma ku Zimbabwe, Morgan Tsvangirai wati akufuna kuti maiko a SADC amutsimikizile za chitetezo chake asanabwelere kwao
 
Read more
Mtsogoleri wa gulu la zigawenga ku Sudan wati apitilira kuputa mzdinda wa Khartoum
Mon, 12 May 2008
Mtsogoleri wa gulu la zigawenga la Justice and Equality Movement – JEM- ku Sudan wati apitilira kuputa mzinda wa Khartoum mpaka boma la dzikolo litagwa
 
Read more
Mgwilizano wa mchipani cha ANC wayamika ganizo la Tsvangirai loimanso pa masankho
Mon, 12 May 2008
Mgwilizano wa chipani cha ANC wayamuika ganizo la Tsvangirai lakuti aime nawo pa masankho achibweleza a president. Mu mgwilizano wa ANC muli a Cosatu, Communist Party ndi ANC
 
Read more
Maiko a DRC ndi Uganda apempha mtsogoleri wa LRA kuti asaine pangano la mtendere
Mon, 12 May 2008
Maiko a DRC ndi Uganda apempha mtsogoleri wa gulu la zigawenga la Lords Resistance Army kuti asaine pangano la mtendere
 
Read more
Chibvomezi chagunduza kumadzulo kwa China
Mon, 12 May 2008
Chibvomelezi chagunduza kumadzulo kwa dziko la China. Chibvomezichi chakukhudza dela la Sichuan limene liri makilometre 92 kuchoka mu mzinda wa Chengdu
 
Read more
Financial Indicators
Shares Total Change
AllShare 32701 53.6%
Resource Unavailable.....
Gold Mining 2472.4 -19.2%
Industrials 25339.6 -147.9%
Financials 17437.7 -124.1%
Information provided by HiSat http://www.hisat.co.za


 
Weather - SouthAfrica
 
Bwelelani kuchiyambi  |  Bungwe la SABC  |  SABC News  |  SABC Africa  |  Cholinga ndi masomphenya  |  Ngodya zathu  |  Malamulo    Mmene mungatipezele  |  Za channel africa  |  Maganizo anu  |  Tsamba lathup
© Tiletsa kukopera izi 1999 -2001 Channel Africa.